1 Samueli 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako anagwada pamapazi+ a Davide ndi kunena kuti: “Zolakwa zonse zikhale pa ine+ mbuyanga. Chonde, lolani kapolo wanu wamkazi alankhule nanu+ ndipo mvetserani mawu a kapolo wanu. Miyambo 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuleza mtima kumanyengerera mtsogoleri wa asilikali, ndipo lilime lofatsa likhoza kuthyola fupa.+
24 Kenako anagwada pamapazi+ a Davide ndi kunena kuti: “Zolakwa zonse zikhale pa ine+ mbuyanga. Chonde, lolani kapolo wanu wamkazi alankhule nanu+ ndipo mvetserani mawu a kapolo wanu.