Genesis 44:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano Yuda anayandikira kwa Yosefe n’kunena kuti: “Chonde mbuyanga, ndapota nanu. Lolani kuti kapolo wanune ndinene mawu amodzi okha.+ Chonde musandipsere mtima,+ pakuti inu muli ngati Farao+ yemwe. 2 Samueli 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno mkaziyo anati: “Ndiloleni ine mtumiki wanu,+ chonde, ndilankhule mawu amodzi+ kwa inu mbuyanga mfumu.” Mfumu inamuuza kuti: “Lankhula!”+
18 Tsopano Yuda anayandikira kwa Yosefe n’kunena kuti: “Chonde mbuyanga, ndapota nanu. Lolani kuti kapolo wanune ndinene mawu amodzi okha.+ Chonde musandipsere mtima,+ pakuti inu muli ngati Farao+ yemwe.
12 Ndiyeno mkaziyo anati: “Ndiloleni ine mtumiki wanu,+ chonde, ndilankhule mawu amodzi+ kwa inu mbuyanga mfumu.” Mfumu inamuuza kuti: “Lankhula!”+