Genesis 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma iye anapitiriza kuti: “Chonde Yehova, musandipsere mtima,+ koma ndiloleni ndilankhulebe.+ Nanga atapezeka 30?” Iye anayankha kuti: “Sindiwononga ndikapezamo 30.”
30 Koma iye anapitiriza kuti: “Chonde Yehova, musandipsere mtima,+ koma ndiloleni ndilankhulebe.+ Nanga atapezeka 30?” Iye anayankha kuti: “Sindiwononga ndikapezamo 30.”