Miyambo 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Wosafulumira kukwiya n’ngozindikira zinthu kwambiri,+ koma wokwiya msanga amalimbikitsa uchitsiru.+ Miyambo 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kuzindikira kumachititsa munthu kubweza mkwiyo wake,+ ndipo kunyalanyaza cholakwa kumam’chititsa kukhala wokongola.+ Miyambo 29:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu olankhula modzitama amabutsa mkwiyo wa mzinda,+ koma anthu anzeru amaletsa mkwiyo.+
29 Wosafulumira kukwiya n’ngozindikira zinthu kwambiri,+ koma wokwiya msanga amalimbikitsa uchitsiru.+
11 Kuzindikira kumachititsa munthu kubweza mkwiyo wake,+ ndipo kunyalanyaza cholakwa kumam’chititsa kukhala wokongola.+