Genesis 50:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho musachite mantha. Ine ndipitiriza kukugawirani chakudya limodzi ndi ana anu.”+ Anawalimbikitsa n’kuwatsimikizira motero. Mateyu 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yesu anayankha kuti: “Ndikukuuza kuti, osati nthawi 7 zokha ayi, koma, Mpaka nthawi 77.+ Aefeso 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma khalani okomerana mtima,+ achifundo chachikulu,+ okhululukirana ndi mtima wonse, monga mmene inunso Mulungu anakukhululukirani ndi mtima wonse kudzera mwa Khristu.+
21 Choncho musachite mantha. Ine ndipitiriza kukugawirani chakudya limodzi ndi ana anu.”+ Anawalimbikitsa n’kuwatsimikizira motero.
32 Koma khalani okomerana mtima,+ achifundo chachikulu,+ okhululukirana ndi mtima wonse, monga mmene inunso Mulungu anakukhululukirani ndi mtima wonse kudzera mwa Khristu.+