Genesis 47:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kumeneko, Yosefe anali kugawira chakudya bambo ake, abale ake ndi banja lonse la bambo ake,+ malinga ndi kuchuluka kwa ana.+ 1 Petulo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Osabwezera choipa pa choipa+ kapena chipongwe pa chipongwe,+ koma m’malomwake muzidalitsa,+ chifukwa anakuitanirani njira ya moyo imeneyi, kuti mudzalandire dalitso.
12 Kumeneko, Yosefe anali kugawira chakudya bambo ake, abale ake ndi banja lonse la bambo ake,+ malinga ndi kuchuluka kwa ana.+
9 Osabwezera choipa pa choipa+ kapena chipongwe pa chipongwe,+ koma m’malomwake muzidalitsa,+ chifukwa anakuitanirani njira ya moyo imeneyi, kuti mudzalandire dalitso.