Aroma 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pitirizani kudalitsa anthu amene amakuzunzani.+ Muzidalitsa,+ osatemberera ayi.+ 1 Akorinto 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ndipo tikugwirabe ntchito yolimba+ ndi manja athu.+ Pamene akutinenera zachipongwe, timadalitsa.+ Pozunzidwa, timapirira.+
12 ndipo tikugwirabe ntchito yolimba+ ndi manja athu.+ Pamene akutinenera zachipongwe, timadalitsa.+ Pozunzidwa, timapirira.+