Salimo 109:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Alekeni anditemberere,+Koma inu mundipatse madalitso.+Iwo aimirira kuti andiukire koma inu muwachititse manyazi,+Ndipo ine mtumiki wanu ndisangalale.+ Aroma 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pitirizani kudalitsa anthu amene amakuzunzani.+ Muzidalitsa,+ osatemberera ayi.+ 1 Petulo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Osabwezera choipa pa choipa+ kapena chipongwe pa chipongwe,+ koma m’malomwake muzidalitsa,+ chifukwa anakuitanirani njira ya moyo imeneyi, kuti mudzalandire dalitso.
28 Alekeni anditemberere,+Koma inu mundipatse madalitso.+Iwo aimirira kuti andiukire koma inu muwachititse manyazi,+Ndipo ine mtumiki wanu ndisangalale.+
9 Osabwezera choipa pa choipa+ kapena chipongwe pa chipongwe,+ koma m’malomwake muzidalitsa,+ chifukwa anakuitanirani njira ya moyo imeneyi, kuti mudzalandire dalitso.