Luka 6:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pitirizani kudalitsa okutembererani ndi kupempherera amene akukunyozani.+ 1 Akorinto 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ndipo tikugwirabe ntchito yolimba+ ndi manja athu.+ Pamene akutinenera zachipongwe, timadalitsa.+ Pozunzidwa, timapirira.+
12 ndipo tikugwirabe ntchito yolimba+ ndi manja athu.+ Pamene akutinenera zachipongwe, timadalitsa.+ Pozunzidwa, timapirira.+