Machitidwe 7:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Kenako anagwada pansi ndi kufuula ndi mawu amphamvu kuti: “Yehova, musawaimbe mlandu wa tchimo ili.”+ Atanena zimenezi anagona tulo ta imfa. Aroma 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pitirizani kudalitsa anthu amene amakuzunzani.+ Muzidalitsa,+ osatemberera ayi.+
60 Kenako anagwada pansi ndi kufuula ndi mawu amphamvu kuti: “Yehova, musawaimbe mlandu wa tchimo ili.”+ Atanena zimenezi anagona tulo ta imfa.