1 Akorinto 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ndipo tikugwirabe ntchito mwakhama ndi manja athu.+ Akamatinenera zachipongwe, timadalitsa+ ndipo akamatizunza, timapirira moleza mtima.+
12 ndipo tikugwirabe ntchito mwakhama ndi manja athu.+ Akamatinenera zachipongwe, timadalitsa+ ndipo akamatizunza, timapirira moleza mtima.+