Aroma 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pitirizani kudalitsa anthu amene akukuzunzani.+ Muzidalitsa, osati kutemberera.+ 1 Petulo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu akakuchitirani choipa musamabwezere ndi choipa,+ akakuchitirani chipongwe musamabwezere ndi chipongwe.+ Mʼmalomwake muziwachitira zabwino*+ chifukwa Mulungu anakusankhani kuti muzidalitsa ena kuti nayenso adzakudalitseni.
9 Munthu akakuchitirani choipa musamabwezere ndi choipa,+ akakuchitirani chipongwe musamabwezere ndi chipongwe.+ Mʼmalomwake muziwachitira zabwino*+ chifukwa Mulungu anakusankhani kuti muzidalitsa ena kuti nayenso adzakudalitseni.