Machitidwe 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo popeza kuti ntchito yawo inali imodzi, anakhala kunyumba kwawoko. Iwo ankagwira ntchito pamodzi,+ pakuti onse anali amisiri opanga mahema. Machitidwe 20:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Inunso mukudziwa bwino kuti manja awa anagwira ntchito kuti ndipeze zosowa zanga+ ndi za amene ali nane. 2 Atesalonika 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 kapena kudya chakudya cha wina aliyense kwaulere.+ M’malomwake, mwa ntchito yathu imene tinagwira mwakhama ndi thukuta lathu,+ tinagwira ntchito usiku ndi usana kuti aliyense wa inu asatilipirire kanthu kalikonse pofuna kutithandiza.+
3 Ndipo popeza kuti ntchito yawo inali imodzi, anakhala kunyumba kwawoko. Iwo ankagwira ntchito pamodzi,+ pakuti onse anali amisiri opanga mahema.
34 Inunso mukudziwa bwino kuti manja awa anagwira ntchito kuti ndipeze zosowa zanga+ ndi za amene ali nane.
8 kapena kudya chakudya cha wina aliyense kwaulere.+ M’malomwake, mwa ntchito yathu imene tinagwira mwakhama ndi thukuta lathu,+ tinagwira ntchito usiku ndi usana kuti aliyense wa inu asatilipirire kanthu kalikonse pofuna kutithandiza.+