Machitidwe 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo popeza kuti ntchito yawo inali imodzi, anakhala kunyumba kwawoko. Iwo ankagwira ntchito pamodzi,+ pakuti onse anali amisiri opanga mahema. 1 Akorinto 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ndipo tikugwirabe ntchito yolimba+ ndi manja athu.+ Pamene akutinenera zachipongwe, timadalitsa.+ Pozunzidwa, timapirira.+
3 Ndipo popeza kuti ntchito yawo inali imodzi, anakhala kunyumba kwawoko. Iwo ankagwira ntchito pamodzi,+ pakuti onse anali amisiri opanga mahema.
12 ndipo tikugwirabe ntchito yolimba+ ndi manja athu.+ Pamene akutinenera zachipongwe, timadalitsa.+ Pozunzidwa, timapirira.+