Miyambo 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Wosafulumira kukwiya n’ngozindikira zinthu kwambiri,+ koma wokwiya msanga amalimbikitsa uchitsiru.+ Miyambo 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu wopsa mtima amayambitsa mkangano,+ koma munthu wosakwiya msanga amaziziritsa mkangano.+ Miyambo 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Munthu wosakwiya msanga ndi wabwino kuposa munthu wamphamvu,+ ndipo munthu wolamulira mtima wake amaposa munthu wogonjetsa mzinda.+ Yakobo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense akhale wofulumira kumva, wodekha polankhula,+ wosafulumira kukwiya,+
29 Wosafulumira kukwiya n’ngozindikira zinthu kwambiri,+ koma wokwiya msanga amalimbikitsa uchitsiru.+
32 Munthu wosakwiya msanga ndi wabwino kuposa munthu wamphamvu,+ ndipo munthu wolamulira mtima wake amaposa munthu wogonjetsa mzinda.+
19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense akhale wofulumira kumva, wodekha polankhula,+ wosafulumira kukwiya,+