Miyambo 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chidani n’chimene chimayambitsa mikangano,+ koma chikondi chimaphimba machimo onse.+ Miyambo 29:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munthu wokonda kukwiya amayambitsa mkangano,+ ndipo aliyense wokonda kupsa mtima amakhala ndi machimo ambiri.+
22 Munthu wokonda kukwiya amayambitsa mkangano,+ ndipo aliyense wokonda kupsa mtima amakhala ndi machimo ambiri.+