Miyambo 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu wopsa mtima amayambitsa mkangano,+ koma munthu wosakwiya msanga amaziziritsa mkangano.+ Yakobo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi nkhondo zimene zikuchitika pakati panu zikuchokera kuti? Nanga kukangana pakati panu kukuchokera kuti? Kodi sizikuchokera m’zilakolako za thupi lanu+ zimene zikuchita nkhondo m’ziwalo zanu?+
4 Kodi nkhondo zimene zikuchitika pakati panu zikuchokera kuti? Nanga kukangana pakati panu kukuchokera kuti? Kodi sizikuchokera m’zilakolako za thupi lanu+ zimene zikuchita nkhondo m’ziwalo zanu?+