Yakobo 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma ngati m’mitima mwanu muli nsanje yaikulu+ ndi kukonda mikangano,+ musadzitamande+ pakuti kutero n’kunamizira choonadi.+
14 Koma ngati m’mitima mwanu muli nsanje yaikulu+ ndi kukonda mikangano,+ musadzitamande+ pakuti kutero n’kunamizira choonadi.+