1 Yohane 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndikukulemberani izi, osati chifukwa chakuti simudziwa choonadi,+ koma chifukwa chakuti mukuchidziwa,+ ndiponso chifukwa chakuti palibe bodza lililonse limene limachokera m’choonadi.+
21 Ndikukulemberani izi, osati chifukwa chakuti simudziwa choonadi,+ koma chifukwa chakuti mukuchidziwa,+ ndiponso chifukwa chakuti palibe bodza lililonse limene limachokera m’choonadi.+