Miyambo 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wophimba machimo akufunafuna chikondi,+ ndipo amene amangokhalira kulankhula za nkhani inayake amalekanitsa mabwenzi apamtima.+ 1 Akorinto 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chikondi+ n’choleza mtima+ ndiponso n’chokoma mtima.+ Chikondi sichichita nsanje,+ sichidzitama,+ sichidzikuza,+ 1 Petulo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koposa zonse, khalani okondana kwambiri,+ pakuti chikondi chimakwirira machimo ochuluka.+
9 Wophimba machimo akufunafuna chikondi,+ ndipo amene amangokhalira kulankhula za nkhani inayake amalekanitsa mabwenzi apamtima.+
4 Chikondi+ n’choleza mtima+ ndiponso n’chokoma mtima.+ Chikondi sichichita nsanje,+ sichidzitama,+ sichidzikuza,+