Akolose 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Musalole kuti munthu aliyense amene amasangalala ndi kudzichepetsa kwachinyengo komanso ndi kulambira angelo akumanitseni+ mphotoyo.+ Anthu oterowo amaumirira zinthu zimene aona ndipo maganizo awo ochimwa amawachititsa kudzitukumula popanda chifukwa chomveka. 1 Petulo 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chimodzimodzinso inu anyamata. Muzigonjera+ amuna achikulire. Koma nonsenu muzichitirana zinthu modzichepetsa,+ chifukwa Mulungu amatsutsa odzikweza, koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.+
18 Musalole kuti munthu aliyense amene amasangalala ndi kudzichepetsa kwachinyengo komanso ndi kulambira angelo akumanitseni+ mphotoyo.+ Anthu oterowo amaumirira zinthu zimene aona ndipo maganizo awo ochimwa amawachititsa kudzitukumula popanda chifukwa chomveka.
5 Chimodzimodzinso inu anyamata. Muzigonjera+ amuna achikulire. Koma nonsenu muzichitirana zinthu modzichepetsa,+ chifukwa Mulungu amatsutsa odzikweza, koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.+