Miyambo 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chidani n’chimene chimayambitsa mikangano,+ koma chikondi chimaphimba machimo onse.+ Miyambo 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wophimba machimo akufunafuna chikondi,+ ndipo amene amangokhalira kulankhula za nkhani inayake amalekanitsa mabwenzi apamtima.+ 1 Akorinto 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chimakwirira zinthu zonse,+ chimakhulupirira zinthu zonse,+ chimayembekezera zinthu zonse,+ chimapirira zinthu zonse.+
9 Wophimba machimo akufunafuna chikondi,+ ndipo amene amangokhalira kulankhula za nkhani inayake amalekanitsa mabwenzi apamtima.+
7 Chimakwirira zinthu zonse,+ chimakhulupirira zinthu zonse,+ chimayembekezera zinthu zonse,+ chimapirira zinthu zonse.+