Miyambo 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chidani n’chimene chimayambitsa mikangano,+ koma chikondi chimaphimba machimo onse.+ 1 Petulo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koposa zonse, khalani okondana kwambiri,+ pakuti chikondi chimakwirira machimo ochuluka.+