1 Akorinto 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chikondi sichitha.+ Koma kaya pali mphatso za kunenera, zidzatha. Kaya kulankhula malilime, kudzatha. Ngakhale mphatso ya kudziwa zinthu, idzatha.+ Akolose 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma kuwonjezera pa zonsezi, valani chikondi,+ pakuti chimagwirizanitsa anthu mwamphamvu+ kwambiri kuposa chinthu china chilichonse.
8 Chikondi sichitha.+ Koma kaya pali mphatso za kunenera, zidzatha. Kaya kulankhula malilime, kudzatha. Ngakhale mphatso ya kudziwa zinthu, idzatha.+
14 Koma kuwonjezera pa zonsezi, valani chikondi,+ pakuti chimagwirizanitsa anthu mwamphamvu+ kwambiri kuposa chinthu china chilichonse.