1 Akorinto 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chikondi sichitha.+ Koma kaya pali mphatso za kunenera, zidzatha. Kaya kulankhula malilime, kudzatha. Ngakhale mphatso ya kudziwa zinthu, idzatha.+ Aefeso 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muziyesetsa ndi mtima wonse kusunga umodzi wathu pokhala mwamtendere umene uli ngati chomangira chotigwirizanitsa. Umodziwo timaupeza mothandizidwa ndi mzimu woyera.+
8 Chikondi sichitha.+ Koma kaya pali mphatso za kunenera, zidzatha. Kaya kulankhula malilime, kudzatha. Ngakhale mphatso ya kudziwa zinthu, idzatha.+
3 Muziyesetsa ndi mtima wonse kusunga umodzi wathu pokhala mwamtendere umene uli ngati chomangira chotigwirizanitsa. Umodziwo timaupeza mothandizidwa ndi mzimu woyera.+