Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 15:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 kuti nonse pamodzi,+ ndi pakamwa pamodzi, mulemekeze Mulungu, Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu.

  • 1 Akorinto 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsopano ndikukudandaulirani+ abale, m’dzina+ la Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti nonse muzilankhula mogwirizana ndi kuti pasakhale magawano+ pakati panu, koma kuti mukhale ogwirizana+ pokhala ndi mtima umodzi ndi maganizo amodzi.+

  • Afilipi 1:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Chachikulu, makhalidwe anu akhale oyenera+ uthenga wabwino wa Khristu. Kuti kaya ndabwera kudzakuonani kapena pamene ine kulibe, ndizimva za inu, kuti mukulimbikira mu mzimu umodzi. Ndipo ndi mtima umodzi,+ mukulimbika pamodzi chifukwa cha chikhulupiriro cha uthenga wabwino.

  • Akolose 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Komanso, mtendere+ wa Khristu ulamulire m’mitima+ yanu, popeza munaitanidwa ku mtenderewo monga ziwalo za thupi limodzi.+ Ndiponso, sonyezani kuti ndinu oyamikira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena