Aroma 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano ndikukudandaulirani abale, kuti musamale ndi anthu amene amayambitsa magawano+ ndi kuchita zinthu zokhumudwitsa ena. Zimenezi ndi zosemphana ndi chiphunzitso+ chimene munaphunzira, choncho muziwapewa.+ Aefeso 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muziyesetsa ndi mtima wonse kusunga umodzi wathu pokhala mwamtendere umene uli ngati chomangira chotigwirizanitsa. Umodziwo timaupeza mothandizidwa ndi mzimu woyera.+
17 Tsopano ndikukudandaulirani abale, kuti musamale ndi anthu amene amayambitsa magawano+ ndi kuchita zinthu zokhumudwitsa ena. Zimenezi ndi zosemphana ndi chiphunzitso+ chimene munaphunzira, choncho muziwapewa.+
3 Muziyesetsa ndi mtima wonse kusunga umodzi wathu pokhala mwamtendere umene uli ngati chomangira chotigwirizanitsa. Umodziwo timaupeza mothandizidwa ndi mzimu woyera.+