Aroma 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano, Mulungu amene amatipatsa mphamvu kuti tithe kupirira ndiponso amene amatitonthoza, achititse nonsenu kukhala ndi maganizo+ amene Khristu Yesu anali nawo, 2 Akorinto 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pomalizira abale, ndikuti pitirizani kukondwera, kusintha maganizo anu, kulimbikitsidwa,+ kukhala ndi maganizo ogwirizana,+ ndiponso kukhala mwamtendere.+ Mukatero, Mulungu wachikondi ndi wamtendere+ adzakhala nanu.
5 Tsopano, Mulungu amene amatipatsa mphamvu kuti tithe kupirira ndiponso amene amatitonthoza, achititse nonsenu kukhala ndi maganizo+ amene Khristu Yesu anali nawo,
11 Pomalizira abale, ndikuti pitirizani kukondwera, kusintha maganizo anu, kulimbikitsidwa,+ kukhala ndi maganizo ogwirizana,+ ndiponso kukhala mwamtendere.+ Mukatero, Mulungu wachikondi ndi wamtendere+ adzakhala nanu.