2 Akorinto 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pomalizira abale, ndikuti pitirizani kukondwera, kusintha maganizo anu, kulimbikitsidwa,+ kukhala ndi maganizo ogwirizana,+ ndiponso kukhala mwamtendere.+ Mukatero, Mulungu wachikondi ndi wamtendere+ adzakhala nanu. Afilipi 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 chititsani chimwemwe changa kusefukira pokhala ndi maganizo amodzi,+ ndi chikondi chofanana. Mukhalenso ogwirizana mu mzimu umodzi, ndi mtima umodzi.+
11 Pomalizira abale, ndikuti pitirizani kukondwera, kusintha maganizo anu, kulimbikitsidwa,+ kukhala ndi maganizo ogwirizana,+ ndiponso kukhala mwamtendere.+ Mukatero, Mulungu wachikondi ndi wamtendere+ adzakhala nanu.
2 chititsani chimwemwe changa kusefukira pokhala ndi maganizo amodzi,+ ndi chikondi chofanana. Mukhalenso ogwirizana mu mzimu umodzi, ndi mtima umodzi.+