2 Akorinto 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 N’chifukwa chake ndikulemba zinthu zimenezi pamene sindili kumeneko, kuti ndikadzakhalako ndisadzagwiritse ntchito ulamuliro wanga mwamphamvu,+ chifukwa Ambuye anandipatsa ulamulirowu kuti ndizikulimbikitsani,+ osati kukufooketsani.
10 N’chifukwa chake ndikulemba zinthu zimenezi pamene sindili kumeneko, kuti ndikadzakhalako ndisadzagwiritse ntchito ulamuliro wanga mwamphamvu,+ chifukwa Ambuye anandipatsa ulamulirowu kuti ndizikulimbikitsani,+ osati kukufooketsani.