1 Akorinto 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kodi mukufuna chiyani? Mukufuna ndibwere kwa inu ndi chikwapu,+ kapena ndi chikondi ndi mzimu wofatsa?+ 2 Akorinto 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komanso ndife okonzeka kupereka chilango pa aliyense wosamvera,+ inuyo mukadzasonyeza kuti ndinu omvera pa chilichonse.+
21 Kodi mukufuna chiyani? Mukufuna ndibwere kwa inu ndi chikwapu,+ kapena ndi chikondi ndi mzimu wofatsa?+
6 Komanso ndife okonzeka kupereka chilango pa aliyense wosamvera,+ inuyo mukadzasonyeza kuti ndinu omvera pa chilichonse.+