1 Timoteyo 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ena mwa amenewa ndi Hemenayo+ ndi Alekizanda,+ ndipo ndawapereka kwa Satana+ kuti akalangidwa,* aphunzire kuti sayenera kulankhula zonyoza Mulungu.+ Aheberi 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti bambo athu otiberekawo, kwa masiku ochepa anali kutilanga malinga ndi zimene anaziona kuti n’zoyenera,+ koma Mulungu amatilanga kuti tipindule ndiponso kuti tikhale oyera ngati iyeyo.+
20 Ena mwa amenewa ndi Hemenayo+ ndi Alekizanda,+ ndipo ndawapereka kwa Satana+ kuti akalangidwa,* aphunzire kuti sayenera kulankhula zonyoza Mulungu.+
10 Pakuti bambo athu otiberekawo, kwa masiku ochepa anali kutilanga malinga ndi zimene anaziona kuti n’zoyenera,+ koma Mulungu amatilanga kuti tipindule ndiponso kuti tikhale oyera ngati iyeyo.+