Miyambo 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wopanduka amawononga mnzake ndi pakamwa pake,+ koma anthu olungama amapulumutsidwa chifukwa chodziwa zinthu.+ Machitidwe 13:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ayuda ataona khamu la anthulo, anachita nsanje+ ndipo anayamba kutsutsa mwamwano zimene Paulo anali kulankhula.+
9 Wopanduka amawononga mnzake ndi pakamwa pake,+ koma anthu olungama amapulumutsidwa chifukwa chodziwa zinthu.+
45 Ayuda ataona khamu la anthulo, anachita nsanje+ ndipo anayamba kutsutsa mwamwano zimene Paulo anali kulankhula.+