2 Akorinto 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti ngakhale nditati ndidzitamandire+ mopitirirako muyezo za ulamuliro umene Ambuye anatipatsa kuti tikulimbikitseni, osati kukupasulani,+ sindingachite manyazi. 2 Akorinto 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 N’chifukwa chake ndikulemba zinthu zimenezi pamene sindili kumeneko, kuti ndikadzakhalako ndisadzagwiritse ntchito ulamuliro wanga mwamphamvu,+ chifukwa Ambuye anandipatsa ulamulirowu kuti ndizikulimbikitsani,+ osati kukufooketsani.
8 Pakuti ngakhale nditati ndidzitamandire+ mopitirirako muyezo za ulamuliro umene Ambuye anatipatsa kuti tikulimbikitseni, osati kukupasulani,+ sindingachite manyazi.
10 N’chifukwa chake ndikulemba zinthu zimenezi pamene sindili kumeneko, kuti ndikadzakhalako ndisadzagwiritse ntchito ulamuliro wanga mwamphamvu,+ chifukwa Ambuye anandipatsa ulamulirowu kuti ndizikulimbikitsani,+ osati kukufooketsani.