Aroma 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chikondi+ sichilimbikitsa munthu kuchitira zoipa mnzake,+ chotero chilamulo chimakwaniritsidwa m’chikondi.+ 1 Yohane 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Lamulo lake ndi lakuti, tikhale ndi chikhulupiriro m’dzina la Mwana wake Yesu Khristu+ ndiponso tizikondana,+ monga mmene iye anatilamulira.
10 Chikondi+ sichilimbikitsa munthu kuchitira zoipa mnzake,+ chotero chilamulo chimakwaniritsidwa m’chikondi.+
23 Lamulo lake ndi lakuti, tikhale ndi chikhulupiriro m’dzina la Mwana wake Yesu Khristu+ ndiponso tizikondana,+ monga mmene iye anatilamulira.