Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 11:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mudzi umakwezedwa chifukwa cha madalitso a anthu olungama,+ koma umagwetsedwa chifukwa cha pakamwa pa anthu oipa.+

  • Machitidwe 19:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Pamenepo mumzindawo munadzaza chisokonezo, ndipo onse pamodzi anathamangira m’bwalo la masewera, atagwira Gayo ndi Arisitako n’kuwakokera m’bwalomo. Gayo ndi Arisitako+ anali anzake a Paulo amene anali kuyenda naye ndipo kwawo kunali ku Makedoniya.

  • Yakobo 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Lilimenso ndi moto.+ Mwa ziwalo zathu zonse, lilime ndilo lili lodzaza ndi zosalungama chifukwa limadetsa thupi lonse.+ Lili ndi moto wa Gehena* ndipo limayatsa moyo wonse wa munthu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena