Machitidwe 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amene anatsagana naye pa ulendowu anali Sopaturo+ mwana wa Puro wa ku Bereya, Arisitako+ ndi Sekundo a ku Tesalonika, Gayo wa ku Debe, ndi Timoteyo,+ koma ochokera m’chigawo cha Asia anali Tukiko+ ndi Terofimo.+ Akolose 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Arisitako+ mkaidi mnzanga akuti moni nonse. Komanso Maliko+ msuweni* wa Baranaba, (amene ndinakulangizani kuti mumulandire+ nthawi iliyonse akadzafika kwa inu,) Filimoni 24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Antchito anzanga, Maliko, Arisitako,+ Dema+ ndi Luka nawonso akupereka moni.
4 Amene anatsagana naye pa ulendowu anali Sopaturo+ mwana wa Puro wa ku Bereya, Arisitako+ ndi Sekundo a ku Tesalonika, Gayo wa ku Debe, ndi Timoteyo,+ koma ochokera m’chigawo cha Asia anali Tukiko+ ndi Terofimo.+
10 Arisitako+ mkaidi mnzanga akuti moni nonse. Komanso Maliko+ msuweni* wa Baranaba, (amene ndinakulangizani kuti mumulandire+ nthawi iliyonse akadzafika kwa inu,)