Machitidwe 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa ulendowu anali limodzi ndi Sopaturo mwana wa Puro wa ku Bereya, Arisitako+ ndi Sekundo a ku Tesalonika, Gayo wa ku Debe ndi Timoteyo,+ koma ochokera mʼchigawo cha Asia anali Tukiko+ ndi Terofimo.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:4 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 167-168 Nsanja ya Olonda,3/15/2001, tsa. 317/15/1998, tsa. 7
4 Pa ulendowu anali limodzi ndi Sopaturo mwana wa Puro wa ku Bereya, Arisitako+ ndi Sekundo a ku Tesalonika, Gayo wa ku Debe ndi Timoteyo,+ koma ochokera mʼchigawo cha Asia anali Tukiko+ ndi Terofimo.+