Machitidwe 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iwo ananena zimenezi chifukwa tsiku lina anaona Terofimo+ wa ku Efeso ali naye limodzi mumzindawo ndiye anaganiza kuti Paulo analowetsa Terofimo mʼkachisi. 2 Timoteyo 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Erasito+ anatsala ku Korinto, koma Terofimo+ ndinamusiya akudwala ku Mileto.
29 Iwo ananena zimenezi chifukwa tsiku lina anaona Terofimo+ wa ku Efeso ali naye limodzi mumzindawo ndiye anaganiza kuti Paulo analowetsa Terofimo mʼkachisi.