Machitidwe 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa ulendowu anali limodzi ndi Sopaturo mwana wa Puro wa ku Bereya, Arisitako+ ndi Sekundo a ku Tesalonika, Gayo wa ku Debe ndi Timoteyo,+ koma ochokera mʼchigawo cha Asia anali Tukiko+ ndi Terofimo.+ 2 Timoteyo 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Erasito+ anatsala ku Korinto, koma Terofimo+ ndinamusiya akudwala ku Mileto.
4 Pa ulendowu anali limodzi ndi Sopaturo mwana wa Puro wa ku Bereya, Arisitako+ ndi Sekundo a ku Tesalonika, Gayo wa ku Debe ndi Timoteyo,+ koma ochokera mʼchigawo cha Asia anali Tukiko+ ndi Terofimo.+