Machitidwe 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ku Adiramutiyo tinakwera ngalawa imene inali pafupi kunyamuka ulendo wopita kumalo osiyanasiyana a m’mphepete mwa nyanja m’chigawo cha Asia. Kenako tinanyamuka, tilinso limodzi ndi Arisitako,+ yemwe anali Mmakedoniya wa ku Tesalonika.
2 Ku Adiramutiyo tinakwera ngalawa imene inali pafupi kunyamuka ulendo wopita kumalo osiyanasiyana a m’mphepete mwa nyanja m’chigawo cha Asia. Kenako tinanyamuka, tilinso limodzi ndi Arisitako,+ yemwe anali Mmakedoniya wa ku Tesalonika.