Machitidwe 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iwo ananena zimenezi chifukwa tsiku lina anaona Terofimo+ wa ku Efeso ali naye limodzi mumzindawo. Atawaona anaganiza kuti Paulo analowetsa Terofimo m’kachisi. 2 Timoteyo 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Erasito+ anatsalira ku Korinto,+ koma Terofimo+ ndinamusiya akudwala ku Mileto.+
29 Iwo ananena zimenezi chifukwa tsiku lina anaona Terofimo+ wa ku Efeso ali naye limodzi mumzindawo. Atawaona anaganiza kuti Paulo analowetsa Terofimo m’kachisi.