Machitidwe 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iwo ananena zimenezi chifukwa tsiku lina anaona Terofimo+ wa ku Efeso ali naye limodzi mumzindawo ndiye anaganiza kuti Paulo analowetsa Terofimo mʼkachisi. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:29 Nsanja ya Olonda,12/15/2001, ptsa. 22-23
29 Iwo ananena zimenezi chifukwa tsiku lina anaona Terofimo+ wa ku Efeso ali naye limodzi mumzindawo ndiye anaganiza kuti Paulo analowetsa Terofimo mʼkachisi.