Machitidwe 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iwo ananena zimenezi chifukwa tsiku lina anaona Terofimo+ wa ku Efeso ali naye limodzi mumzindawo. Atawaona anaganiza kuti Paulo analowetsa Terofimo m’kachisi.
29 Iwo ananena zimenezi chifukwa tsiku lina anaona Terofimo+ wa ku Efeso ali naye limodzi mumzindawo. Atawaona anaganiza kuti Paulo analowetsa Terofimo m’kachisi.