Machitidwe 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amene anatsagana naye pa ulendowu anali Sopaturo+ mwana wa Puro wa ku Bereya, Arisitako+ ndi Sekundo a ku Tesalonika, Gayo wa ku Debe, ndi Timoteyo,+ koma ochokera m’chigawo cha Asia anali Tukiko+ ndi Terofimo.+ 2 Timoteyo 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Erasito+ anatsalira ku Korinto,+ koma Terofimo+ ndinamusiya akudwala ku Mileto.+
4 Amene anatsagana naye pa ulendowu anali Sopaturo+ mwana wa Puro wa ku Bereya, Arisitako+ ndi Sekundo a ku Tesalonika, Gayo wa ku Debe, ndi Timoteyo,+ koma ochokera m’chigawo cha Asia anali Tukiko+ ndi Terofimo.+