Aefeso 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano, kuti mudziwenso mmene zinthu zikuyendera pa moyo wanga ndi mmene ine ndilili, Tukiko,+ m’bale wokondedwa ndiponso mtumiki wokhulupirika mwa Ambuye, adzakufotokozerani zonse.+ Akolose 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tukiko,+ m’bale wanga wokondedwa komanso mtumiki wokhulupirika, ndi kapolo mnzanga mwa Ambuye, adzakudziwitsani zonse za ine. 2 Timoteyo 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Tukiko+ ndamutuma ku Efeso.
21 Tsopano, kuti mudziwenso mmene zinthu zikuyendera pa moyo wanga ndi mmene ine ndilili, Tukiko,+ m’bale wokondedwa ndiponso mtumiki wokhulupirika mwa Ambuye, adzakufotokozerani zonse.+
7 Tukiko,+ m’bale wanga wokondedwa komanso mtumiki wokhulupirika, ndi kapolo mnzanga mwa Ambuye, adzakudziwitsani zonse za ine.