Akolose 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tukiko+ amene ndi mʼbale wanga wokondedwa, mtumiki wokhulupirika komanso kapolo mnzanga mwa Ambuye, adzakuuzani zonse zokhudza ine. Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:7 Nsanja ya Olonda,7/15/1998, tsa. 8
7 Tukiko+ amene ndi mʼbale wanga wokondedwa, mtumiki wokhulupirika komanso kapolo mnzanga mwa Ambuye, adzakuuzani zonse zokhudza ine.