Akolose 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tukiko,+ m’bale wanga wokondedwa komanso mtumiki wokhulupirika, ndi kapolo mnzanga mwa Ambuye, adzakudziwitsani zonse za ine. Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:7 Nsanja ya Olonda,7/15/1998, tsa. 8
7 Tukiko,+ m’bale wanga wokondedwa komanso mtumiki wokhulupirika, ndi kapolo mnzanga mwa Ambuye, adzakudziwitsani zonse za ine.