Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 19:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Pamenepo mumzindawo munadzaza chisokonezo, ndipo onse pamodzi anathamangira m’bwalo la masewera, atagwira Gayo ndi Arisitako n’kuwakokera m’bwalomo. Gayo ndi Arisitako+ anali anzake a Paulo amene anali kuyenda naye ndipo kwawo kunali ku Makedoniya.

  • Machitidwe 27:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ku Adiramutiyo tinakwera ngalawa imene inali pafupi kunyamuka ulendo wopita kumalo osiyanasiyana a m’mphepete mwa nyanja m’chigawo cha Asia. Kenako tinanyamuka, tilinso limodzi ndi Arisitako,+ yemwe anali Mmakedoniya wa ku Tesalonika.

  • Akolose 4:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Arisitako+ mkaidi mnzanga akuti moni nonse. Komanso Maliko+ msuweni* wa Baranaba, (amene ndinakulangizani kuti mumulandire+ nthawi iliyonse akadzafika kwa inu,)

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena