Akolose 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Luka,+ dokotala wokondedwa, akuti moni nonse. Dema+ nayenso akuti moni. 2 Timoteyo 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti Dema+ wandisiya chifukwa chokonda zinthu za m’nthawi* ino,+ ndipo wapita ku Tesalonika. Keresike wapita ku Galatiya,+ ndipo Tito wapita ku Dalimatiya.
10 Pakuti Dema+ wandisiya chifukwa chokonda zinthu za m’nthawi* ino,+ ndipo wapita ku Tesalonika. Keresike wapita ku Galatiya,+ ndipo Tito wapita ku Dalimatiya.